Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera pamodzi ndi mayi wa fuko lino Madam Monica Chakwera akuyembekezeka kukhala nawo pa mapemphero a misa pa mpingo wa katolika wa St. Peters mu mzinda wa Mzuzu.
Mtsogoleri wa dziko linoyu akuyembekezeka kufika pa mpingowu cha m’ma 10 koloko m’mawa uno.
Olemba: Jackson Sichali.