Oyimba nyimbo za uzimu, Favoured Martha, wapereka thandizo la yunifomu kwa ana 23 ovutika apa sukulu ya pulaimale ya Chilobwe ku Blantyre. Katswiriyu analimbikitsanso oyimba...
Katswiri ochita zisudzo m’dziko muno Jamil Chikakuda ndipo amatchuka ndi dzina loti Che Mandota wati mphoto ya MBC Entertainers of Year ndiyo ya phindu kuposa...
Kampani ya Serato Media Group, imene yakhala ikuthandiza kugulitsa nyimbo za Zeze Kingston, yathetsa m’gwirizano ndi oyimbayu patatha zaka zinayi akugwira ntchito limodzi. Kalata yochokera...
Some of the country’s models have said the slow growth of their industry is largely due to a widespread misunderstanding about the goals and purpose...
Gospel Musician, Mike Alibewawoh, has emphasised the need for artists to create music that inspires hope and resilience in the face of life’s challenges. He...
Eni kampani yopanga sopo ya Hirwa General Dealers ati agoma ndi mmene akugwilira ntchito kazembe wawo watsopano, Emmie Deebo. Akuluakulu akampaniyi ati ntchito yomwe Emmie...
Maso Awards has announced its intentions to launch an arts export initiative in a bid to ship out local art through collaboration with international and...