Oyimba nyimbo zauzimu Steve Wazisomo Muliya wati nyimbo zotchyakuka bwino zitha kuthandiza kuchepetsa imfa za anthu amene amadzipha chifukwa cha nkhawa. Muliya, amene anapambana chaka...
Hip-hop artist Phyzix says he has finally dismissed those that labelled his music as “bubblegum” after receiving K5 million in royalties from the Copyright Society...
Oyimba nyimbo za uzimu, mayi busa Mary Thuya, ati chimbale chimene akutulutsa chotchedwa “Ndathokoza” ayimba pothokoza Mulungu kaamba kowachiritsa ku matenda a Covid-19. A Thuya...
Organisers of this year’s Tumaini Festival have revealed that South Africa’s Reggae icon Maverick Mavo and Ntunya will star at the 10th anniversary festival alongside...
Malawian artist Onesimus faces formidable competition in this year’s Zikomo Africa Awards’ Artist of the Year category. He has been nominated along with 23 other...
Oyimba nyimbo za uzimu, Favoured Martha, wapereka thandizo la yunifomu kwa ana 23 ovutika apa sukulu ya pulaimale ya Chilobwe ku Blantyre. Katswiriyu analimbikitsanso oyimba...
The Presidential Charity Golf Initiative continues to attract corporate support as the National Bank of Malawi has today pumped K10 Million into the initiative Speaking...
Kampani ya Serato Media Group, imene yakhala ikuthandiza kugulitsa nyimbo za Zeze Kingston, yathetsa m’gwirizano ndi oyimbayu patatha zaka zinayi akugwira ntchito limodzi. Kalata yochokera...