Apolisi athandiza pantchito yothana ndi mikangano yokhudza malo – Gumba
Nduna yazamalo a Deus Gumba atsindika kufunika kogwira ntchito limodzi ndi apolisi pantchito yolimbana ndi kuthetsa mikangano yokhudza malo m’dziko muno. Ndunayi yanena izi ku

