Eni galimoto akondwa ndi dongosolo lokonza msewu wa Makanjira
Bungwe la Transporters Association of Malawi lati kukonza msewu wa Mangochi-Makanjira kudzathandizanso kwambiri kulimbikitsa ntchito za mtengatenga ndi malonda pakati pa dziko lino ndi la

