Olembankhani ndi mlatho wazochitika ku nyumba ya malamulo — CSAT
Bungwe la Centre for Social Accountability & Transparency (CSAT) lati ndi koyenera kuti olembankhani azidziwa komanso kutsatira bwino momwe nyumba ya malamulo (Parliament) imagwilira ntchito

