MERA ichenjeza eni malo omwetsera mafuta omwe sakutsata malamulo
Bungwe loona zamphamvu ndinso mafuta agalimoto m’dziko muno la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) lachenjeza eni kampani amalo omwetsera mafuta kuti atseka malowa ngati sakutsata

