‘Tidziyamba ndife aMalawi kutsatsa malonda a dziko lathu’
Mtsogoleri wadziko lino, Dr Lazarus Chakwera, wati dziko lino silikuchita bwino kwenikweni chifukwa choti timataya nthawi ndikufalitsa zinthu zoononga mbiri yathu m’malo mofalitsa zambiri zabwino...

