Asilikali akufunafunabe ndege yomwe inanyamula wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino ku Chikangawa
Asilikali ankhondo adziko lino a MDF, pamodzi ndi nthambi zina za chitetezo, akufunafunabe ku Chikangawa m’boma la Mzimba ndege yomwe inanyamula wachiwiri kwa mtsogoleri wa...

