Asiya zolemba, akufuna ku nyumba ya malamulo
Pamene ntchito yokonzekera chisankho chapa 16 September ikuyandikira, tsopano zadziwika kuti atolankhani odziwika bwino opitilira khumi ndi asanu-15 awonetsa chidwi pa ndale ndipo akonzeka kudzapikisana...

