Ndalama zokwana K80.4 million ndi zomwe zapezeka pa masewero amu ligi ya TNM apakati pa matimu a FCB Nyasa Big Bullets komanso Mighty Mukuru Wanderers...
Brands Africa says it will continue to give back to its customers who have developed loyalty to the firm’s products. Marketing Manager for Brands Africa,...
Bungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo m’dziko muno la FAM lati likupanga chothekera kuti lidzikhala mu ubale wabwino ndi kampani komanso anthu ochita za...
Timu ya Dedza Dynamos tsopano izidziwika kuti Premeir Bet Dedza Dynamos kutsatira m’gwirizano umene yakhazikitsa ndi kampani ya Premier Bet wa ndalama zokwana K100 million...
Katswiri wampira wamiyendo wa asungwana wadziko lino, Tabitha Chawinga,amene akusewerera timu ya PSG ku France, amusankha kukhala osewera amene wakankha chikopa mododometsa mu ligi yakumeneko...
The 2024 Region 5 Youth Games has included new sporting codes of Karate and Table Tennis, replacing Gymnastics and Taekwondo. Stanley Mutoya, Region 5 CEO,...
UK-based Malawian forward, Shaquille Gwengwe, currently playing for Dorchester Town, has garnered recognition by clinching the 23/24 Golden Boot Award in the Southern League Premier...
Katswiri wa nkhonya m’dziko muno, Alexander ‘Cage’ Likande, wamwalira m’bandakucha wa lero pangozi ya njinga yamoto yomwe inaombana ndi galimoto. Malinga ndi zimene akunena mnzake...