Pakufunika ndondomeko zoyenera zopewera ngozi zogwa mwadzidzidzi —- DODMA
DoDMA, yomwe ndi nthambi yoona za ngozi zakugwa mwadzidzidzi, yatsindikiza za kufunika kwa ndondomeko zopewera ngozi zobwera kaamba ka kusintha kwa nyengo. Malinga ndi m’modzi...

