Dziko la Malawi lili ndi mwai waukulu woonjezera Mphamvu zamagetsi
Nduna yoona zamphamvu zamagetsi, a Ibrahim Matola, yomwe imachita nawo msonkhano waukulu wamaiko apa dziko lonse wokambirana zamphamvu zamagetsi wa World Energy Congress ku Rotterdam...

