Category : Sports
Timu ya Hilltop Socials yawina chikho cha under 21 ku Mzuzu
Akuluakulu oyendetsa zamasewero mchigawo chakumpoto ati akhwimitsa malamulo kuti matimu amene akusewera mu chikho cha Mzuzu FAM under 21 League akhale okhawo amene ndi achisodzera...
Tyson Fury wasiya nkhonya
Katswiri omenya nkhonya m’dziko la England, Tyson Fury, walengeza kuti wasiya masewerowa, malinga ndi nyumba yofalitsa nkhani ya BBC. Nkhonya yake yomaliza ya katswiriyu, amene...
Kefasi wa Cobbe Barracks ndi katswiri pa mpikisano othamanga wa asilikali
Kefasi Chitsala waku Cobbe Barracks ku Zomba ndi yemwe wakhala katswiri wampikisano wa chaka chino wa asilikali a m’dziko muno wothamanga mtunda wa ma kilomita...

