Tidzayika zipilala, sitinatseke barrage – Water Authority
Bungwe la National Water Resources Authority lati lili ndi mapulani omanga zipilala zomwe zithandize kuletsa anthu kumanga zinthu zosiyanasiyana m’phepete mwanyanja. Mkulu wabungweli, a Dwight...