Author : Charles Pensulo
352 Posts -
0 Comments
Unduna wazantchito watseka mbali ina ya Makandi Tea Estate
Unduna wa zantchito, watseka mbali ina ya Makandi Tea Estate imene ili m’boma la Thyolo chifukwa chophwanya ena mwa malamulo antchito. Mbaliyi ndi kumene kuli...
Bambo amangidwa atapha mwana omupeza
Apolisi ya Nathenje m’boma la Lilongwe amanga a Luwashi Bakali, 26, powaganizira kuti apha mwana omupeza wazaka ziwiri. Izi zachitika m’mudzi wa Kawale kwa mfumu...
Ophunzira pa UNIMA akhazikitsa kampani ya luso lamakono
Ophunzira pa sukulu yaukachenjede ya University of Malawi(Unima) ku Zomba akhazikitsa chipangizo chothandiza anthu omwe ali ndi ulumali wosaona. Mmodzi mwa ophunzirawo, Hudson Mwangalika, wati...
Chileka Police officers inspire learners
Chileka Police Station has urged learners at Lipunga Primary School in Blanytre to work hard so that they become reliable future citizens. Led by Superintendent...
Business community empowers police
South West Police Region has commended the business community in the region for supporting them in strengthening security ahead of the festive season. Commissioner of...
Madzi aukhondo afika ku Mphampha ndi Tsambalabooka m’boma la Chikwawa
Anthu a midzi ya Mphampha ndi Tsambalabooka kwa mfumu yaikulu Lundu ku Chikwawa ati ndi okondwa kuti tsopano adzimwa madzi aukhondo. Anthuwa anena izi kampani...
Namondwe Chido wakula mphamvu
Nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya DoDMA yati anthu m’dziko muno akhale tcheru komanso atsatire malangizo malinga ndi malipoti okhudza namondwe Chido amene akuyenda...
MET predicts heavy rains in Blantyre
Department of Climate Change and Meteorological Services (MET) has forecast erratic rainfall in Blantyre this month, with continuous normal to above-normal rainfall expected to begin...