Amai ena akhumudwisa mpingo
Amai ena apa mpingo wina m’dera la Mayaka m’boma la Zomba akhumudwitsa mamembala apa mpingowo.
Chindeu chibuka pakati pa mamuna ndi azimayi awiri
Chindeu cha mtima bii chinabuka pakati pa mwamuna wina ndi azimayi awiri m’dera la mfumu Machinjiri mboma la Blantyre.
Mwamuna wanchiuno avulalitsa mkazi wa chibwenzi
Mwamuna wina wa mchiuno wapa mudzi wa Chiphe kwa Kachere m’boma la Dedza wavulalitsa chibwenzi chake cha nseri.
Banja litha dzuwa likuswa mtengo
Mai wina mdera la Kasisi m’boma la Chikwawa manja ali ku nkhongo banja lake litatha dzuwa likuswa mtengo.