Mkazi agenda mwamuna wake ndi mwala
Mwamuna wina kwa Mayaka mboma la Zomba ali pa ululu woopsya kwambili mkazi wake atamuvulaza pomugenda ndi mwala ku nkhongo.
Mwambo wamapemphero usokonekela
Mwambo wamapemphero a chitsitsimutso wasokonezeka ku Nchalo m’boma la Chikwawa.
Asiidwa banja kamba kosakhulupilika
Mkulu wina mboma la Salima manja ali ku nkhongo mwamuna wake atamusasa kuti sakumufunanso banja kamba kosakhulupirika.
Chidakwa chisekesa anthu
Chidakwa china mdera la Makwangwala m’boma la Ntcheu chinaseketsa anthu. Nkhaniyi ikuti mwamunayo anakwatila zaka zitatu zapitazo ndipo wakhala ali pa chikamwini mderalo.