Dalaivala ayenda zamadulira atagulisa engine
Dalaivala wina ku Chilomoni mu mzinda wa Blantyre akuti wathawa ndipo akungoyendayenda mtchire powopa achitetezo omwe akumufunafuna pomuganizira kuti agulitsa engine ya galimoto yomwe amayendera.
Gogo wina auka kwa akufa
Anthu akwa Gunda mdera la Jenala ku Phalombe akukhala mwa mantha chifukwa cha zomwe zawachitikira.
Mai wina adzelezeka
Mai wina m’dera la Khonsolo m’boma la Mzimba wadzelezeka. Nkhaniyi ikuti mderalo muli mai wina yemwe ali pa banja ndipoi amakhala pamudzi wa mwamuna wake.
Akunthidwa kamba koyika nyama ya pusi mu kanyenya
Mkulu wina wogulitsa kanyenya ku Malosa mboma la Zomba waona zakuda zitadziwika kuti amasakaniza kanyenya wa mbuzi ndi nyama ya pusi.