Banja lina ndi nyakwawa ina mdera la Malili ku Lilongwe akuyang’anizana ndi diso la mkhwezule.
Mai wina ku Blantyre akuyenda mogwetsa nkhope yake pansi chifukwa cha manyazi.
Agogo awili okalamba kwambili akunthana kwambili kwa Mchinguza mboma la Machinga mpaka kutsala pang’ono kusokoneza mwambo wachinamwali cha jando.
Achinyamata ena anai ku Maleule kwa Kapeni m’boma la Blantyre anawamangilira pa mtengo ku manda kamba kosokoneza pa maliro.