Paja pali mau oti magwiragwira amapha manja.
Kambelembele wina aona zakuda pa sitolo zapa Santhe kwa mfumu yaikulu Kalolo m’boma la Lilongwe.
Omvera paja pali mau oti magwiragwira amapha manja. Nkhaniyi yapherezera mdera la Mzukuzuku ku Mzimba pamene mnyamata wina wayamba kulankhula zosamveka atakaba mtondo wapa banja lina.
Mwamuna wina kwa Ganya m’boma la Ntcheu zamusokonekera mkazi wa chibwezi atamulanda foni.