Aulimali ayamika ndondomeko yopereka ndalama za mtukula pakhomo pa lamya
Anthu aulumali m’boma la Phalombe ayamika boma chifukwa choyamba kupereka ndalama za mtukula pakhomo kudzera pa lamya, zimene zathandiza kuti asamayende mtunda wa utali akafuna...