Author : Paul Mlowoka
160 Posts -
0 Comments
Nico registers a higher return on investment
Despite the business sector being affected by natural disasters and pandemics such as COVID-19, Nico Pensions has through its Ufulu Pension Fund registered increased returns...
‘Malo nawa koma tionepo chitukuko pasanathe zaka ziwiri’
Mwambo opereka malo kwa atsikana osewera mpira wa miyendo mutimu ya Scorchers wayamba ndi kupereka zikalata zaumwini kwa osewerawa ku unduna wa zamalo ku Lilongwe,...
Scorchers lero imwemwetera
Atsikana amene amasewera mpira wamiyendo mu timu yadziko lino ya Scorchers adzuka ndinkhope zowala chifukwa lero boma likuyembekezeka kukwaniritsa zimene mtsogoleri wadziko lino, Dr Lazarus...
NBM sponsors MDF military drill
National Bank of Malawi has donated K 8.8 million to the Malawi Defence Force (MDF)’s 2024 Drill Competition, which is expected to be held at...
Chepetsani chinyengo poweruza milandu — Mzikamanda
Mkulu wa mabwalo a milandu m’dziko muno, Justice Rizine Mzikamanda, walangiza oweruza milandu mumabwalo osiyanasiyana kuti adzilemekeza malumbiro awo pogwira ntchito yawo mwachilungamo. A Mzikamanda...
Bullets yapanga ubale ndi Sun Group
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yasainilana m’gwirizano ndi kampani ya Sun Group imene idzipereka madzi akumwa. Izi zikubwera pamene mkulu oyendetsa ntchito ku Bullets...
Save the Children hands over assets to partners
In an effort to promote girl-child education in the country, Save the Children has donated assorted items worth K800 million to Blantyre and Livingstonia CCAP...
“Tisanaloze zala adindo tidziunike kaye ifeyo”
M’modzi mwa abusa amene amatumikira m’dziko la United Kingdom koma kwawo ndi kuno ku Malawi, Chance Munthari, wati aMalawi akuyenera kusiya kuloza zala ena pamavuto...
Artists unite to address issues affecting their welfare
Artists in the country under the banner Musicians Rights Forum have come together to fight for their rights, with an aim of addressing several challenges...