Author : Foster Maulidi
279 Posts -
0 Comments
Aliyense atenge gawo posamala misika — Khonsolo ya Lilongwe
Khonsolo ya Mzinda wa Lilongwe yapempha mzika zake kukhala adindo pa ntchito yosamala misika yosiyanasiyana ya mumzindawu. Mfumu ya mzinda wa Lilongwe, a Esther Sagawa,...
Area 30 lauds Blue Eagles Volley club for Botswana fundraiser
Malawi Police Service has praised Blue Eagles Volleyball Club for their initiative in raising funds for the forthcoming Zone 6 Senior Championship set for Botswana...
‘Dekhani pa bizinesi’
Achinyamata omwe alandira mpamba wa ndalama zokwana K1 million aliyense kuchokera kwa Triephornia Mpinganjira pansi pa ndondomeko ya ‘kuthandiza omwe alibe kuthekera kupita patsogolo’ awalangiza...
Salima Sugar ikupereka K500 million kwa osamuka m’minda yawo
Kampani ya Salima Sugar ikupereka ndalama zokwana K498 million kwa mabanja 1,000, amene amakhala pa minda ya kampaniyi, ngati chipukuta misonzi kuti asamuke pa malowa....
Achinyamata asamadziyang’anire pansi, watero Belekanyama
Phungu wa dera laku m’mwera kwa Msinja m’boma la Lilongwe, a Francis Belekanyama, wapempha achinyamata kuti asiye kudziyang’anira pansi pazochitika zokhudza ndale m’dziko muno. A...