Malawi Broadcasting Corporation
Agriculture Business Development Local Local News

Salima Sugar yayambanso kupanga Shuga

Kampani ya Salima Sugar yayambiranso kupanga Shuga pamene nyengo yopumira yatha tsopano.

Nyengoyi imakhalapo chaka chilichonse kuyambira mwezi ya November mpaka April.

A Sosten Gwengwe, omwe ndi nduna ya zamalonda, alamula kampaniyi kuti iwonetsetse kuti Shuga wawo akupezeka pa msika ngati njira imodzi yothana ndi vuto lakusowa kwa katunduyi.

Kampaniyi imapanga shuga wochuluka 125 metric tons patsiku, yemwe ndi wa ndalama zokwana K225 million.

Uyu akhala sugar oyamba kupangidwa pa kampaniyi ndi a Malawi chisiyileni mgwirizano ndi kampani ya AUM Sugar and Allied Limited yaku India.

#MBCDigital
#Manthu

 

Print Friendly, PDF & Email

Related posts

Oimba aphunzire kugwira ntchito ndi aluso ena — Billy Kaunda

Emmanuel Chikonso

Tobacco farmers want season to open in March

MBC Online

BRAZILIAN SPECIALIST PLEDGES CATARACT SURGERY FOR 1000 MALAWIANS

MBC Online
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.