Nduna ya zaulimi a Sam Kawale lero ikuyendela ntchito yomanaga ngalande yodutsa madzi aulimi wanthilira pansi pa Shire Valley Transformation Program mboma la Chikwawa.
Ndunayi ayifotokozela kusintha komwe kulipo pama plan omanga ngalandeyi kamba ka Namondwe Ana yemwe anakokolola zomangamanga zina za ntchito yi mchaka cha 2022.
Gawo loyamba lomanga ngalandeyi ifika kumapeto mkatikati mwa chaka cha mawa.
Olemba Chipiliro Mtumodzi