Azimayi ajuga aphwanyisa mnyumba ya mzawo
Anthu okhala ku Area 9 ku Machinjiri mu mzinda wa Blantyre ndiokhumudwa chifukwa cha zomwe achita azimayi ena otchova juga pomphwanyisa nyumba ya mzawo.
Mbava yaikazi ikanidwa kulowa mu golosale
Mai wina kwa TA Msamala mboma la Balaka amuletsa kuti asadzalowenso mu golosale ya banjalo mwamuna wake atazindikira kuti mayiyo ndi mbava.
Asowa mtengo ogwira atagwidwa ndi chibwenzi
Ku Chigumula munzinda wa Blantyre mnyamata wina zinamukoka manja mkazi wake atazindikira kuti mwamuna wakeyo ali ndi chibwenzi cha mseri. Nkhaniyi ikuti mnyamatayo adakwatira mtsikana wa m’dera lina yemwe panopa wakwanitsa zaka zingapo ali mbanja.
Abwenza ndalama poopa kulandidwa katundu
Mkazi wina yemwe mwamuna wake adamwalila posachedwapa wabweza ndalama kwa mwamuna wina yemwe amamuyenda njomba poopa akuchimuna kuti amulanda katundu kwa Mayaka mboma la Zomba.