Mbusa achita zachisembwere ndi mlamu wake
Mbusa wina wabalalitsa nkhosa za chauta kwa T/A Ntuwa mboma la Mchinji zitadziwika kuti anamupezelera akuchita zachisembwere ndi mlamu wake.
Akhumudwa atawona nkhope ya chibwenzi chapa facebook
Mkulu wina yemwe amakhala ku Lilongwe wabwelera manja ali m’khosi pa ulendo wake omwe anapita ku Blantyre kukaonana ndi chibwenzi chake chomwe anachipeza pa FACEBOOK.
Mafumu awiri akunthana pamaliro
Mwambo wa Maliro unasokonezeka mdera la mfumu Mwasambo m’boma la Karonga mafumu awiri atakhuthana koopsya polimbilana kulankhula pa mwambowo.
Agwa padenga posasula Malata kamba ka Nsanje
Mai wina kwa Mwadyawathu m’boma la Kasungu ali mu ulu woopsya atagwa pa denga la nyumba ndikuvulala pamene amasasula Malata chifukwa cha Nsanje.