Mwamuna wina atandala mnyuma kamba ka manyazi
Mwamuna wina mdera la Mazengera m’boma la Lilongwe akukhalira kutandala mnyumba chifukwa cha manyazi ndi zomwe zamuchitikira.
Katswili oyimba za uzimu achita manyazi
M’modzi mwa akatswili oimba nyimbo za uzimu ku Blantyre akuyenda wela-wela ngati nkhuku yogwela mvuwo chifukwa cha manyazi.
Anthu aku Lilongwe akhala mwa mantha
Anthu a mdera la Senior Group Malembe kwa Chitukula mboma la Lilongwe akukhala mwa mantha.
Mai wina atandala mnyumba kamba ka manyazi
Mai wina akukhalira kutandala mnyumba kwa Changoima mdera la Chapananga m’boma la Chikwawa chifukwa cha manyazi.