05
May

05/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 3876 times

Agonana ndi ana awo awirir owapeza
Anthu a m’mudzi wa Malunga Mfumu yayikulu Mponda m’boma la Mangochi ati ndiwokhumudwa kwambiri komanso odana nkhawa ndi zomwe akhala akuchita bamboo wina pogonana ndi ana ake awiri owapeza kwa nthawi yayitali.

05
May

04/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 3217 times

Mkazi wa nyakwawa awilikiza chimasomaso  
Mkazi wa Nyakwawa wina mdera la Chakhadza m’boma la Lilongwe wakhumudwitsa anthu chifukwa cha khalidwe lake lachimasomaso.

05
May

03/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 3408 times

Athesa banja atanamizidwa zaukwati wina
Mayi wina wa mdera la Mfumu Mkanda m’boma la Mchinji manja ali mkhosi atapasula banja lake pomvera mwamuna wina yemwe anamunamiza kuti amukwatira.

05
May

02/05/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 3631 times

Mbusa wamkazi afunsira mlembi wa mpingo
Anthu a mpingo wina ku Nathenje mboma la Lilongwe aleka kupita ku kachisi zitadziwka kuti mbusa wao yemwe ndi wa mkazi amafunsila mlembi wake yemwe ndi wa mwamuna.

Get Your Newsletter