Banja lisokonekela kamba ka kovinisa
Banja lina latekeseka m’dera la Mfumu Mkanda mboma la Mulanje mkulu wina atapeza mkazi wake akuvina ndi mphongo zina m’mudzimo.
Agwira nchiuno mwa munthu odwala
Anthu a m’mudzi mwa Likhonyowa mboma la Machinga anatsala pang’ono kuthidzimula mkulu wina atamuzindikira kuti amagwira nchiuno mwa munthu odwala.
Athyole nthumba ndalama ya eni
Mkulu wina akuyenda mogwetsa nkhope yake pansi chifukwa cha manyazi mu mzinda wa Blantyre atamtulukila kuti anathyolela mthumba ndalama yomwe anamupatsa kuti akasiye ku banki.
Akuluakulu ena apita kumanda kufuna chakudya
Nyakwawa ina ku Chilomoni mu mzinda wa Blantyre yachenjeza adzukulu omwe akumakonda kupita kumanda akaona kuti chakudya chayandikila basi.