Mkamwini athamangitsidwa
Mkamwini wina amuthamangitsa pa banja kwa Gulupu Chinama mdera la Sub traditional Authority Ndanga m’boma la Mulanje.
Banja lina lidabwisa anthu ku Nsanje
Anthu ena mdera la Malemia m’boma la Nsanje ati sakumvetsa ndi zomwe lachita banja lina mderalo.
Mwamuna wina manja ali ku nkhongo kamba ka magalasi
Mwamuna wina ku M’deka m’boma la Blantyre manja ali ku nkhongo ena mwa magalasi a nyumba yake ataswedwa.
Banja lithela ku malo ogonela alendo
Mai wina ku Malimba pa boma la Salima manja ali ku nkhongo banja lake litathera ku malo ogona alendo.