Chithumwa chigwa nchiuno
Mpondamatiki wina kwa M’nyanja m’boma la Kasungu akukhalira kubindikira m’nyumba chifukwa cha manyazi chithumwa cha bizinesi yake chitavuka mchuuno.
Athetsa banja kamba kakhalidwe la nchiuno
Mayi wina kwa Kanyenda m’boma la Nkhota-kota wadabwitsa anthu ndi khalidwe lake la mchuno pothetsa banja lake ndikukalowerera mnyamata wina wolisha n’gombe.
Nkulu wachitetezo akhala mwa mantha
Mkulu wina wodziwika bwino pa nkhani zolimbikitsa chitetezo m’dera la Kaomba mboma la Kasungu akukhala mwa mantha mayi wa m’modzi wa anthu akuba anamangidwa chifukwa cha umbava ataopyseza kuti bamboyo asowa wamoyo.
Akumpingo anyanyala maliro kamba kachakudya
Akulu akulu ampingo wina kwa Ganya m’boma la Ntcheu anyanyala kuyendetsa mwambo wa maliro chifukwa chowamana zakudya.