Zozizwa zichitika gogo wina atamwalira
Anthu a m’dera la Mfumu yayikulu Chadza m’boma la Lilongwe akukhala mwa mantha komanso odabwa pa zodabwitsa zomwe zinachitika , gogo wina atamwalira mderalo.
Awowozedwa pamaliro kamba ka dyera
Oyimila mfumu ina ku Mbayani mu mzinda wa Blantyre akuyenda monyowa achinyamata atawaooza pa maliro chifukwa cha chadyera.
Apasula banja kamba ka mwano
Mtsikana wina ku Chigumula mu mzinda wa Blantyre wapasula banja lake ndi manja ake chifukwa cha mwano.
Ukwati utha kamba kolimbilana ndalama zofupa
Ukwati wina omwe unachitika Lachisanu lapitali ku Bangwe mu mzinda wa Blantyre watha makolo atayamba kulimbilana ndalama ya pelekanipelekani.