Anjatidwa pogwilira ndikupeleka mimba kwa mwana
Apolisi ku Nchalo mboma la Chikwawa agwila ndikutsekera mchitokosi mwamuna wina wa zaka 41 chifukwa choti ati wakhala akugwilira mpaka kupereka mimba kwa mtsikana wa zaka 16, yemwe ndi mwana wake wompeza.
Athidzimulidwa atamupeza akuchita zadama ndimamuna wa mwini
Mayi wina kwa T/A Kuntaja m’boma la Blantyre wachimina atathidzimulidwa kwa chakwanu leka atampezerela akuchita zadama ndi mwamuna wamwini.
Asowa mtendere ndondocha zikumutsatira kulikonse
Bambo wina kwa Ngomano Mfumu yayikulu Thomasi m’boma la Thyolo akusowa mtendere ndondocha zikumakhalira kumutsatila kuli konse akupita.
Asanduka kamba kachimasomaso
Mayi wina m’dera la Mfumu Chadza wanenetsa kuti wasiya khalidwe lake lachimasomaso atasanduka pamene amafika ku nyumba kwake.