Mfumu ithetsa banja kamba ka nsanje
Mfumu yina kwa Nsamala m’boma la Balaka lathetsa banja lake chifukwa cha msanje.
Alandidwa phone kamba kowilikiza zibwenzi
Mkulu wina kwa Kanduku mboma la Mwanza waona mbwadza mkazi wake atamulanda phone ya m’manja chifukwa chowirikiza zibwenzi.
Wamisala azunguza mayi wina kamba kabuluku othina
Mayi wina pa malo okwelera bus yopita ku Mulanje waona ngati malodza wamisala atayamba kumuzazila ati kamba koti anavala buluku lothina.
Omwalira azizitswa anthu ataoneka pagulu la anamfedwa
Mikoko yogona ya m’mudzi wina kwa Chilikumwendo mboma la Dedza maka mudzi omwe wayandikana ndiku Mitundu mboma la Lilongwe yaima mitu m’nyamata wina yemwe anamwalila atamuona ali patsogolo pagulu lomwe linanyamula malilo ake kupita kumanda.