Awilikiza chisembwere ndi ana osapola nchomba
Mayi wina mdera la mfumu Mabuka m’boma la Mulanje akudabwitsa athu powilikiza kuchita zachisembwere ndi ana osapola pa mchombo.
Akana kusegula manda kamba ka ngongole ya malemu
Nyakwawa ina kwa Mphuka m’boma la Thyolo yakhumudwitsa anthu pokana kutsekula ku manda kuti ati malemu womwalirayo wapita ndi ngongole.
Galimoto iwomba fisi odabwisa
Galimoto inaomba fisi wodabwitsa pa mlatho wapa mtsinje wina kwa Santhe m’boma la Kasungu usiku wapitawu.
Azemberana ndi mwana wake obala yekha
Mkulu wina wapa mudzi wa Mtenje kwa Likoswe m’boma la Chiradzulu akubindikira m’nyumba kamba ka manyazi zitadziwika kuti akuzemberana ndi mwana wake wobereka yekha.