You are here:CategoriesNkhani Zam'maboma
27
July

26/07/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 2406 times

Aluma anthu kamba kosemphana maganizo
Mikoko yogona yapa mudzi wina kwa Nkalo mboma la Chiradzulu yadzudzula mkulu wina chifukwa choluma anthu angapo atasemphana maganizo.

27
July

25/07/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 1983 times

Mwana wina aima pakhomo a manda
Anthu apa mudzi wina mboma la Neno aima mitu ndi zomwe anachita mwana wa Nyakwawa ina pokaima pakhomo kumanda ati kudikila chitanda cha bamboo ake.

27
July

24/07/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 1823 times

Achilapa kuti sadzatukwananso
Mai wina wam’mudzi mwa Namalo ku Bangwe mu mzinda wa Blantyre wati wachimina sadzayambilanso kutukwana anzake m’mudzi bwalo litamulipitsa chindapusa cha 10-thousand Kwacha.

27
July

23/07/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 2055 times

Awilikiza kuchita chibwenzi mamuna akuona
Mayi wina wa m’mudzi mwa Nicholas ku Ligowe mboma la Neno akudabwitsa anthu chifukwa chowirikiza kuchita chibwenzi ndi mphongo ina koma mwamuna wake osachitapo kanthu.

About us

Malawi Broadcasting Corporation is a public broadcaster mandated and formed by Government under an Act of Parliament in 1964, to enhance the successful implementation of all its social and economic programs...

Social Media

Catch us on these social networks for more information

Facebook Twitter RSS

Get Your Newsletter