You are here:CategoriesNkhani Zam'maboma
07
August

07/08/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 1840 times

Akomoka ndi mowa kuntchito
Ntchito zinasokonekela pa kampani ina yopanga bisiketi mu mzinda wa Lilongwe mwamuna wina atakomoka ndi mowa.

07
August

06/08/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 1872 times

Afuna kumangililidwa mumtengo akamwalira
Anthu ena mdera la Ndamera mboma la Nsanje akukhala mwa mantha ndi zomwe anachita Gogo wina wokhwima yemwe anauza anthu kuti akadzamwalira asadzalowe m’manda ati m’malo mwake adzangomumangilira mu mtengo.

05
August

05/08/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 2101 times

Mkazi wamitala atentha udzu wa mkazi nzake
Mkazi wina yemwe ali pa mitala pa mudzi Chidula kwa Mangwazu m’boma la Kasungu amulamula kuti alipire mkazi m’nzake katundu komanso mitolo ya udzu 100 yomwe anayitentha.

04
August

04/08/15

Written by
Published in Nkhani Zam'maboma
Read 2286 times

Akuntha mkulu wawo ndi mpini
Anthu apa mudzi wina m’dera la Mfumu Cheku-cheku m’boma la Neno ndi wokhumudwa kwambiri ndi zomwe yachita nyakwawa yawo pokuntha ndi mpini mkulu wabwalo mpaka maganizi kuyendelera ngati madzi.

About us

Malawi Broadcasting Corporation is a public broadcaster mandated and formed by Government under an Act of Parliament in 1964, to enhance the successful implementation of all its social and economic programs...

Social Media

Catch us on these social networks for more information

Facebook Twitter RSS

Get Your Newsletter