You are here:CategoriesNkhani Zam'maboma
25
April

Alanda mkazi wa chimwene

Mnyamata wina ku Mitundu m’boma la Lilongwe walanda mkazi wa mchimwene wake m’boma la Salima. 

20
April

Amugulura mano anai kamba ka mkazi
Mnyamata wina pa sitolo zapa Kamchere m’boma la Mchinji amugulula mano anai polimbirana mkazi.

18
April

Mkulu wina waku Mozambique awopsyeza anthu
Wamalonda wina wa mdziko la Mozambique koma amachita malonda ake pa msika wa Nkando m’boma la Mulanje waopsyeza amalonda anzake kuti adzisowa mmodzi-mmodzi.

12
April

Akunthidwa kamba kogwilira
Mwamuna wina ku Mulanje analira chokweza anthu okwiya atamuthidzimula kolapitsa chifukwa cha nkhani yogwirila.

Page 1 of 119

About us

Malawi Broadcasting Corporation is a public broadcaster mandated and formed by Government under an Act of Parliament in 1964, to enhance the successful implementation of all its social and economic programs...

Social Media

Catch us on these social networks for more information

Facebook Twitter RSS

Get Your Newsletter