You are here:CategoriesNkhani Zam'maboma
23
March

Aba nkhuku za apongozi
Mkamwini wina ku Lizulu m’boma la Ntcheu akuyenda njira zamadulira kamba ka manyazi atamutulukira kuti anaba nkhuku za mpongozi wake.

22
March

Agwilira mkazi wa mwini ku munda

Mkulu wina m’dera la Mfumu Chimwala mboma la Mangochi waziziritsa anthu nkhongono atagwilira mkazi wa mwini kumunda.

21
March

Athawa kutchito kamba ka ngongole
Mkulu wina wathawa ku ntchito kwake chifukwa cha ngongole mdera la Kapoka m’boma la Chitipa.

16
March

Nyakwawa ithawa pa mudzi

Nyakwawa ina yathawa pa mudzi kusiya mudziwo opanda woutsogolera kwa Gulupu Muutcha mfumu Kachenga m’boma la Balaka.

Page 1 of 116

About us

Malawi Broadcasting Corporation is a public broadcaster mandated and formed by Government under an Act of Parliament in 1964, to enhance the successful implementation of all its social and economic programs...

Social Media

Catch us on these social networks for more information

Facebook Twitter RSS

Get Your Newsletter