Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Saulos Chilima, masana ano ali nawo pa mwambo olonga a Benson Chilima kukhala Group Village Headman Chilima ya mdera la Mfumu Njewa ku Lilongwe.
#MBCDigital
#Manthu