Mmodzi wa akulu akulu mchipani cha MCP yemwenso ndi nduna yaza Chitetezo Chadziko a Ken Zikhale Ng’oma ati boma lipitiriza kutukula madera onse a dziko lino mosakondera potukula miyoyo ya anthu.
Mwachitsanzo,iwo anakamba za ntchito ya minda ikulu ikulu ya Mega Farms imene ikugwiridwa ku Machinga.
A Zikhale Ng’oma amayankhula pa bwalo laza masewero la Chaka ku Machinga pa msonkhano omwe anachititsa.
Mu kanema ali m’musiyu, akuonetsa zina zomwe a Ng’oma analankhula.
#MBCOnlineServices