Kampani yofulula mowa ya Castel, yakhazikitsa chakumwa chatsopano chimene akuchitcha kuti Pomme Breeze.
M’modzi mwa akuluakulu a kampaniyi, a Fiona Nyambo, ati chakumwa chaukali chimenechi ndi chozuna komanso chokonzedwa mwa makono.